AmunaNdife - Zangalia

by Lawrence Chinoko
(Malawi, Lilongwe)


Jay kay on the board
( Intro )
Eeee Amuna
Eeeee Amuna
Amuna
(Jay Kay Beatx )

(Verse 1 Wewe)
Tsono girl ndimafuna ndikuMale
Kunyumba kwanga uzikatsuka mbale
Nkazi umandiwaza ukumasekerera
Chikondi muntimamu chikuyenderera
Katundu Olemetsa bwanji n'dzaku dendekera
Kwanu kungatalike bwanji n'dzakusendera
Olo uzizanyanyala n'dzaku nyengerera
Ine Wewe n'dzaku chengetera

Umapita kumwezi kuti ukaphe dzuwa
Sindinganame girl ndiwe chiphadzuwa
Inawo olo adzinyanyala izo ndi zawo
Tiye m'banja girl let's make a vow

(Hook)
Mmodzi, Modzi. Zangalia !
Ndimafuna wanga. Zangalia
Otsuka mbale. Zangalia
Ndimapoto omwe. Zangalia. X2

(Verse 2 L.A.C )
Aaah. Aaaahh
Ndimafuna Nkazi ngati iweee. ZaCareer
Gwedeza thako zungulira
Mmmmmh Kunyada, Osazifila
Ntheradi momwe mmakufunira
Bwera pafupi, pereka moni gwada
Ndikufuna uzikaphika beef osati chigwada
Akazi anzako onse wa murder

Nkazi wa big booty
AmunaNdife kodi ndani sanaigule
Uyundiwanga makape nonse muyenda wabule
Akukamba za shit ndani apa ine ndimubule
Eeeeee

(Hook) X2

(Verse 3 Oscarr)
Ndikufuna changa chinamwali
Chizionekera patali
Chikhale cha figure, Tikamayenda fans izi patuka kumbali
Chizitha kupota miBongo
Chinkazi chozungila Bongo

She must be a bad chick make people Say Ooh,
Ngati loggo ya Opera
Ama be her man , Muzi hopeRa
Kuvetsa kuwawa ngati opera , tsabola
Koma tizivetsana kukoma cause,
Ama be her fella

(Hook)

(Bridge)
Zangalia !!
Zangalia !!
Zangalia. X4

(Outro)
Ndimafuna Nkazi ngati iwe
Ngati Loggo ya Opera
Chikuyenderera

Click here to post comments

Join in and write your own page! It's easy to do. How? Simply click here to return to Post Your Lyrics.